Yohane 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo anamufunsa kuti: “Nanga ndiwe ndani? Ndiwe Eliya kapena?”+ Iye anayankha kuti: “Ayi.” “Kapena ndiwe Mneneri?”+ Iye anayankha kuti: “Ayi!” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:21 Yesu—Ndi Njira, tsa. 30
21 Iwo anamufunsa kuti: “Nanga ndiwe ndani? Ndiwe Eliya kapena?”+ Iye anayankha kuti: “Ayi.” “Kapena ndiwe Mneneri?”+ Iye anayankha kuti: “Ayi!”