Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 18:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova Mulungu wanu adzakupatsani mneneri ngati ine kuchokera pakati pa abale anu, ndipo mudzamumvere mneneri ameneyo.+

  • Yohane 6:14, 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anthuwo ataona chizindikiro chimene anachitacho, anayamba kunena kuti: “Mosakayika uyu ndi mneneri uja amene anati adzabwera padziko.”+ 15 Kenako Yesu atadziwa kuti anthu akufuna kubwera kudzamugwira kuti amuveke ufumu, anachoka+ nʼkupitanso kuphiri yekhayekha.+

  • Yohane 7:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Pa tsiku lomaliza, tsiku lalikulu la chikondwererocho,+ Yesu anaimirira nʼkufuula kuti: “Ngati wina akumva ludzu, abwere kwa ine adzamwe madzi.+

  • Yohane 7:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ena mʼgululo amene anamva mawu amenewa, anayamba kunena kuti: “Ndithu ameneyu ndi Mneneri.”+

  • Machitidwe 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndipotu Mose ananena kuti, ‘Yehova* Mulungu wanu adzakupatsani mneneri ngati ine kuchokera pakati pa abale anu.+ Mudzamumvere pa zinthu zonse zimene adzakuuzeni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena