Yohane 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Asamariya ambiri ochokera mumzindawo anakhulupirira mwa iye chifukwa cha mawu a mayi uja. Mayiyo anachitira umboni kuti: “Iyeyu wandiuza zinthu zonse zimene ndakhala ndikuchita.”+
39 Asamariya ambiri ochokera mumzindawo anakhulupirira mwa iye chifukwa cha mawu a mayi uja. Mayiyo anachitira umboni kuti: “Iyeyu wandiuza zinthu zonse zimene ndakhala ndikuchita.”+