Yohane 4:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kenako anafikanso ku Kana wa ku Galileya, kumene anasandutsa madzi kukhala vinyo kuja.+ Tsopano kumeneku kunali munthu wina amene ankatumikira mfumu, amene mwana wake wamwamuna ankadwala ku Kaperenao.
46 Kenako anafikanso ku Kana wa ku Galileya, kumene anasandutsa madzi kukhala vinyo kuja.+ Tsopano kumeneku kunali munthu wina amene ankatumikira mfumu, amene mwana wake wamwamuna ankadwala ku Kaperenao.