Yohane 5:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu ameneyu anali nyale yoyaka komanso yowala, ndipo kwa kanthawi kochepa inu munali ofunitsitsa kusangalala kwambiri chifukwa cha kuwala kwakeko.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:35 Nsanja ya Olonda,1/15/2005, tsa. 11
35 Munthu ameneyu anali nyale yoyaka komanso yowala, ndipo kwa kanthawi kochepa inu munali ofunitsitsa kusangalala kwambiri chifukwa cha kuwala kwakeko.+