-
Yohane 7:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Chifukwa palibe munthu amene amachita zinthu mwachinsinsi pamene akufuna kudziwika kwa anthu. Ngati inu mumachita zinthu zimenezi, mudzionetsere poyera kudzikoli.”
-