Yohane 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Poyamba ophunzira akewo sanathe kumvetsa zimenezi. Koma Yesu atapatsidwa ulemerero,+ iwo anakumbukira kuti zimene anthuwo anamuchitira zinali zofanana ndendende ndi zimene zinalembedwa zokhudza iyeyo.+
16 Poyamba ophunzira akewo sanathe kumvetsa zimenezi. Koma Yesu atapatsidwa ulemerero,+ iwo anakumbukira kuti zimene anthuwo anamuchitira zinali zofanana ndendende ndi zimene zinalembedwa zokhudza iyeyo.+