-
Yohane 16:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Atanena zimenezi, ena mwa ophunzira akewo anayamba kufunsana kuti: “Kodi akutanthauza chiyani pamene akutiuza kuti, ‘Kwa kanthawi simudzandionanso ndipo kwa kanthawi mudzandiona,’ komanso kuti, ‘chifukwa ndikupita kwa Atateʼ?”
-