-
Yohane 16:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Pamenepo ena mwa ophunzira akewo anayamba kufunsana kuti: “Kodi akutanthauza chiyani mmene akutiuza kuti, ‘Kwa kanthawi simudzandionanso, ndipo kwa kanthawi mudzandiona,’ ndi kuti, ‘chifukwa ndikupita kwa Atate’?”
-