-
Yohane 16:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mayi akamabereka amazunzika kwambiri chifukwa nthawi yake yafika. Koma mwana akabadwa sakumbukiranso kupweteka konse kuja chifukwa chosangalala kuti mwana wabadwa padziko.
-