Yohane 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamene mayi akubereka amazunzika kwambiri, chifukwa nthawi yake yafika.+ Koma mwana akabadwa, sakumbukiranso kupweteka konse kuja chifukwa cha chimwemwe kuti munthu wabadwa padziko.
21 Pamene mayi akubereka amazunzika kwambiri, chifukwa nthawi yake yafika.+ Koma mwana akabadwa, sakumbukiranso kupweteka konse kuja chifukwa cha chimwemwe kuti munthu wabadwa padziko.