Genesis 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kwa mkaziyo, Mulungu ananena kuti: “Ndidzawonjezera kuvutika kwako pamene uli ndi pakati.+ Pobereka ana udzamva zowawa.+ Udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira.”+ Yesaya 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa cha inu Yehova, ife takhala ngati mkazi wapakati amene watsala pang’ono kubereka, amene akumva zowawa za pobereka, amene akulira ndi ululu wa pobereka.+
16 Kwa mkaziyo, Mulungu ananena kuti: “Ndidzawonjezera kuvutika kwako pamene uli ndi pakati.+ Pobereka ana udzamva zowawa.+ Udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira.”+
17 Chifukwa cha inu Yehova, ife takhala ngati mkazi wapakati amene watsala pang’ono kubereka, amene akumva zowawa za pobereka, amene akulira ndi ululu wa pobereka.+