Machitidwe 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pa mavuto amene anakumana nawo, iye anaonekera wamoyo kwa atumwiwo pogwiritsa ntchito maumboni ambiri otsimikizirika.+ Iwo anamuona masiku onse 40 ndipo ankawauza za Ufumu wa Mulungu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:3 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 15-16 Mawu a Mulungu, tsa. 82
3 Pambuyo pa mavuto amene anakumana nawo, iye anaonekera wamoyo kwa atumwiwo pogwiritsa ntchito maumboni ambiri otsimikizirika.+ Iwo anamuona masiku onse 40 ndipo ankawauza za Ufumu wa Mulungu.+