-
Machitidwe 2:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho mkokomowu utamveka, panasonkhana gulu lalikulu la anthu. Iwo anadabwa kwambiri, chifukwa aliyense anawamva akulankhula mʼchilankhulo chake.
-