-
Machitidwe 2:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho mkokomo umenewu utamveka, panasonkhana khamu la anthu ambiri. Iwo anadabwa kwambiri, chifukwa aliyense wa iwo anawamva akulankhula m’chinenero chake.
-