-
Machitidwe 5:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kodi mundawo sunali mʼmanja mwako usanaugulitse? Ndipo utaugulitsa, ndalamazo sukanatha kuchita nazo zilizonse zimene ukufuna? Ndiye nʼchifukwa chiyani unaganiza zochita zinthu zimenezi? Apatu sunanamize anthu, koma Mulungu.”
-