Machitidwe 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi mundawo sunali m’manja mwako usanaugulitse? Ndipo utaugulitsa, kodi ndalamazo sukanatha kuchita nazo mmene ukanafunira? N’chifukwa chiyani mumtima mwako unaganiza zochita zinthu zimenezi? Pamenepa sikuti wanamiza+ anthu ayi, koma Mulungu.”+
4 Kodi mundawo sunali m’manja mwako usanaugulitse? Ndipo utaugulitsa, kodi ndalamazo sukanatha kuchita nazo mmene ukanafunira? N’chifukwa chiyani mumtima mwako unaganiza zochita zinthu zimenezi? Pamenepa sikuti wanamiza+ anthu ayi, koma Mulungu.”+