-
Machitidwe 5:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Nthawi yomweyo Safira anagwa pansi pafupi ndi mapazi a Petulo nʼkufa. Pamene anyamata aja ankalowa anamʼpeza atafa kale. Choncho anamunyamula nʼkutuluka naye ndipo anakamuika mʼmanda pafupi ndi mwamuna wake.
-