Machitidwe 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi yomweyo anagwa pansi pamapazi a Petulo n’kumwalira.+ Pamene anyamata aja amalowa anam’peza atafa kale. Choncho anamunyamula ndi kutuluka naye kukamuika m’manda pafupi ndi mwamuna wake.
10 Nthawi yomweyo anagwa pansi pamapazi a Petulo n’kumwalira.+ Pamene anyamata aja amalowa anam’peza atafa kale. Choncho anamunyamula ndi kutuluka naye kukamuika m’manda pafupi ndi mwamuna wake.