-
Machitidwe 5:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Chifukwa mʼmasiku amʼmbuyomu, kunali Teuda amene anadzitchukitsa kwambiri ndipo anthu pafupifupi 400 analowa mʼgulu lake. Koma anaphedwa, ndipo onse amene ankamutsatira anabalalika, osapezekanso.
-