Machitidwe 5:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Chifukwa m’masiku am’mbuyomu, kunali Teuda amene anadzitchukitsa kwambiri+ ndipo amuna pafupifupi 400 analowa m’gulu lake.+ Koma anaphedwa, ndipo onse amene anali kumutsatira anabalalitsidwa osaonekanso.
36 Chifukwa m’masiku am’mbuyomu, kunali Teuda amene anadzitchukitsa kwambiri+ ndipo amuna pafupifupi 400 analowa m’gulu lake.+ Koma anaphedwa, ndipo onse amene anali kumutsatira anabalalitsidwa osaonekanso.