Machitidwe 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma pamene anamusiya yekha,+ mwana wamkazi wa Farao anamutenga nʼkumamulera ngati mwana wake.+