Machitidwe 7:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Choncho Mulungu anawasiya kuti atumikire magulu akumwamba+ ngati mmene malemba amanenera mʼbuku la Aneneri. Malembawo amati, ‘Anthu inu a nyumba ya Isiraeli, kodi mʼchipululu muja munkapereka kwa ine nsembe ndi zopereka zina kwa zaka 40? Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:42 Nsanja ya Olonda,11/15/2000, ptsa. 14-15
42 Choncho Mulungu anawasiya kuti atumikire magulu akumwamba+ ngati mmene malemba amanenera mʼbuku la Aneneri. Malembawo amati, ‘Anthu inu a nyumba ya Isiraeli, kodi mʼchipululu muja munkapereka kwa ine nsembe ndi zopereka zina kwa zaka 40?