Machitidwe 7:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Inutu munkanyamula chihema cha Moloki+ ndi nyenyezi ya mulungu wotchedwa Refani, mafano amene munapanga kuti muziwalambira. Choncho ndidzakuthamangitsirani kutali kupitirira ku Babulo.’+
43 Inutu munkanyamula chihema cha Moloki+ ndi nyenyezi ya mulungu wotchedwa Refani, mafano amene munapanga kuti muziwalambira. Choncho ndidzakuthamangitsirani kutali kupitirira ku Babulo.’+