Machitidwe 7:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Inutu munali kunyamula chihema cha Moloki+ ndi nyenyezi+ ya mulungu Refani, mafano amene munapanga kuti muziwalambira. Chotero ndidzakupitikitsirani+ kutali kupitirira Babulo.’
43 Inutu munali kunyamula chihema cha Moloki+ ndi nyenyezi+ ya mulungu Refani, mafano amene munapanga kuti muziwalambira. Chotero ndidzakupitikitsirani+ kutali kupitirira Babulo.’