-
Machitidwe 10:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndiyeno anawalowetsa mʼnyumba nʼkuwasamalira monga alendo ake.
Kutacha, ananyamuka nʼkupita nawo ndipo abale ena a ku Yopa anapita naye limodzi.
-