-
Machitidwe 10:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndiyeno anawalowetsa m’nyumba ndi kuwachereza.
M’mawa mwake ananyamuka ndi kupita nawo, ndipo abale ena a mu Yopa anatsagana naye.
-