Machitidwe 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Petulo anamudzutsa nʼkunena kuti: “Imirira, inenso ndine munthu ngati iwe wemwe.”+