Machitidwe 10:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 osati anthu onse, koma mboni zimene Mulungu anasankhiratu, zomwe ndi ifeyo, amene tinadya ndiponso kumwa naye limodzi ataukitsidwa.+
41 osati anthu onse, koma mboni zimene Mulungu anasankhiratu, zomwe ndi ifeyo, amene tinadya ndiponso kumwa naye limodzi ataukitsidwa.+