Machitidwe 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthu amenewa apereka miyoyo yawo chifukwa cha dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu.+