-
Machitidwe 16:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno usiku Paulo anaona masomphenya. Anaona munthu wina wa ku Makedoniya ataima nʼkumuuza kuti: “Wolokerani ku Makedoniya kuno mudzatithandize.”
-