Machitidwe 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno usiku Paulo anaona masomphenya.+ Munthu wina wa ku Makedoniya anaimirira ndi kumupempha kuti: “Wolokerani ku Makedoniya kuno mudzatithandize.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:9 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 126 Nsanja ya Olonda,1/15/2012, ptsa. 9-10
9 Ndiyeno usiku Paulo anaona masomphenya.+ Munthu wina wa ku Makedoniya anaimirira ndi kumupempha kuti: “Wolokerani ku Makedoniya kuno mudzatithandize.”