Yobu 33:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye amawalankhula m’maloto+ ndi m’masomphenya+ a usiku,Anthu akakhala m’tulo tofa nato,Akamagona pabedi.+ Machitidwe 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mu Damasiko munali wophunzira wina dzina lake Hananiya.+ Ndiyeno Ambuye analankhula naye m’masomphenya kuti: “Hananiya!” Iye anayankha kuti: “Ine, Ambuye.” 2 Akorinto 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyenera kudzitama. Zoona, kudzitama si kopindulitsa. Koma tiyeni tisiye kaye nkhani imeneyi, tipite ku nkhani yokhudza masomphenya+ ndi mauthenga ochokera kwa Ambuye.
15 Iye amawalankhula m’maloto+ ndi m’masomphenya+ a usiku,Anthu akakhala m’tulo tofa nato,Akamagona pabedi.+
10 Mu Damasiko munali wophunzira wina dzina lake Hananiya.+ Ndiyeno Ambuye analankhula naye m’masomphenya kuti: “Hananiya!” Iye anayankha kuti: “Ine, Ambuye.”
12 Ndiyenera kudzitama. Zoona, kudzitama si kopindulitsa. Koma tiyeni tisiye kaye nkhani imeneyi, tipite ku nkhani yokhudza masomphenya+ ndi mauthenga ochokera kwa Ambuye.