Machitidwe 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Woyangʼanira ndende uja atadzuka nʼkuona kuti zitseko za ndende nʼzotseguka, anasolola lupanga lake kuti adziphe, poganiza kuti akaidiwo athawa.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:27 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, ptsa. 16-175/15/1990, tsa. 25
27 Woyangʼanira ndende uja atadzuka nʼkuona kuti zitseko za ndende nʼzotseguka, anasolola lupanga lake kuti adziphe, poganiza kuti akaidiwo athawa.+