-
Machitidwe 16:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Choncho woyangʼanira ndende uja anauza Paulo uthengawo kuti: “Akuluakulu a zamalamulo atumiza anthu kudzanena kuti awirinu mumasulidwe. Choncho tulukani tsopano, ndipo mupite mwamtendere.”
-