-
Machitidwe 16:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Choncho woyang’anira ndende uja anauza Paulo uthengawo, kuti: “Akuluakulu a boma atumiza anthu kudzanena kuti awirinu mumasulidwe. Choncho tulukani tsopano, ndipo mupite mu mtendere.”
-