Machitidwe 16:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma Paulo anawauza kuti: “Iwo atikwapula pamaso pa anthu nʼkutitsekera mʼndende popanda kutizenga mlandu, chikhalirecho ndife Aroma.+ Kodi tsopano akutitulutsa mwamseri? Ayi, zimenezo sizitheka! Abwere eniakewo adzatitulutse okha.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:37 Nsanja ya Olonda,3/1/2015, tsa. 126/15/1990, ptsa. 16-17
37 Koma Paulo anawauza kuti: “Iwo atikwapula pamaso pa anthu nʼkutitsekera mʼndende popanda kutizenga mlandu, chikhalirecho ndife Aroma.+ Kodi tsopano akutitulutsa mwamseri? Ayi, zimenezo sizitheka! Abwere eniakewo adzatitulutse okha.”