Machitidwe 16:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno asilikaliwo anakanena zimenezi kwa akuluakulu a zamalamulo aja. Akuluakulu a zamalamulowo anachita mantha atamva kuti anthuwo ndi Aroma.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:38 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 131
38 Ndiyeno asilikaliwo anakanena zimenezi kwa akuluakulu a zamalamulo aja. Akuluakulu a zamalamulowo anachita mantha atamva kuti anthuwo ndi Aroma.+