Machitidwe 16:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma iwo atatuluka mʼndendemo anapita kunyumba kwa Lidiya. Ataona abale anawalimbikitsa,+ kenako ananyamuka nʼkumapita. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:40 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 132 Nsanja ya Olonda,9/15/1996, tsa. 28
40 Koma iwo atatuluka mʼndendemo anapita kunyumba kwa Lidiya. Ataona abale anawalimbikitsa,+ kenako ananyamuka nʼkumapita.