Machitidwe 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Paulo anati: “Ubatizo umene Yohane ankabatiza anthu unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Ankauza anthu kuti akhulupirire amene akubwera mʼmbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:4 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 110 Yesu—Ndi Njira, tsa. 30
4 Kenako Paulo anati: “Ubatizo umene Yohane ankabatiza anthu unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Ankauza anthu kuti akhulupirire amene akubwera mʼmbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.”