Machitidwe 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Paulo anati: “Yohane anabatiza anthu ubatizo umene unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Anali kuuza anthu kuti akhulupirire amene anali kubwera m’mbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:4 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 110 Yesu—Ndi Njira, tsa. 30
4 Pamenepo Paulo anati: “Yohane anabatiza anthu ubatizo umene unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Anali kuuza anthu kuti akhulupirire amene anali kubwera m’mbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.”