Mateyu 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inetu ndikukubatizani m’madzi+ chifukwa cha kulapa kwanu,+ koma amene akubwera+ m’mbuyo mwanga ndi wamphamvu kuposa ine, ndipo sindili woyenera kumuvula nsapato zake.+ Ameneyo adzakubatizani ndi mzimu woyera+ komanso ndi moto.+ Maliko 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yohane m’batizi anafika m’chipululu, ndipo anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Machitidwe 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa Yohane anabatizadi ndi madzi, koma pasanathe masiku ambiri mudzabatizidwa ndi mzimu woyera.”+
11 Inetu ndikukubatizani m’madzi+ chifukwa cha kulapa kwanu,+ koma amene akubwera+ m’mbuyo mwanga ndi wamphamvu kuposa ine, ndipo sindili woyenera kumuvula nsapato zake.+ Ameneyo adzakubatizani ndi mzimu woyera+ komanso ndi moto.+
4 Yohane m’batizi anafika m’chipululu, ndipo anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+
5 Chifukwa Yohane anabatizadi ndi madzi, koma pasanathe masiku ambiri mudzabatizidwa ndi mzimu woyera.”+