Maliko 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anali kulalikira kuti: “Pambuyo pangapa pakubwera winawake wamphamvu kuposa ine; ine sindili woyenera kuwerama ndi kumasula zingwe za nsapato zake.+ Yohane 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye ndiye amene akubwera m’mbuyo mwangamu. Komabe, zingwe za nsapato zake ine sindili woyenera kuzimasula.”+ Machitidwe 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma pamene Yohane anali kukwaniritsa utumiki wake, anali kunena kuti, ‘Kodi mukuganiza kuti ine ndine ndani? Amene inu mukumuganizira si ine ayi. Koma wina akubwera pambuyo panga, amene ine sindili woyenera kumumasula nsapato kumapazi kwake.’+
7 Iye anali kulalikira kuti: “Pambuyo pangapa pakubwera winawake wamphamvu kuposa ine; ine sindili woyenera kuwerama ndi kumasula zingwe za nsapato zake.+
27 Iye ndiye amene akubwera m’mbuyo mwangamu. Komabe, zingwe za nsapato zake ine sindili woyenera kuzimasula.”+
25 Koma pamene Yohane anali kukwaniritsa utumiki wake, anali kunena kuti, ‘Kodi mukuganiza kuti ine ndine ndani? Amene inu mukumuganizira si ine ayi. Koma wina akubwera pambuyo panga, amene ine sindili woyenera kumumasula nsapato kumapazi kwake.’+