Yohane 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 (Yohane anachitira umboni za iye, moti anali kuchita kufuula kuti: “Amene akubwera m’mbuyo mwangamu wandipitirira ine, chifukwa anakhalapo ine ndisanabadwe.”)+ Yohane 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Uyu ndi amene ndinali kunena uja kuti, M’mbuyo mwanga mukubwera munthu wina amene wandipitirira ine, chifukwa anakhalapo ine ndisanabadwe.+
15 (Yohane anachitira umboni za iye, moti anali kuchita kufuula kuti: “Amene akubwera m’mbuyo mwangamu wandipitirira ine, chifukwa anakhalapo ine ndisanabadwe.”)+
30 Uyu ndi amene ndinali kunena uja kuti, M’mbuyo mwanga mukubwera munthu wina amene wandipitirira ine, chifukwa anakhalapo ine ndisanabadwe.+