Yohane 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 (Yohane anachitira umboni za iye, moti anali kuchita kufuula kuti: “Amene akubwera m’mbuyo mwangamu wandipitirira ine, chifukwa anakhalapo ine ndisanabadwe.”)+ Yohane 8:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Yesu anati: “Ndithudi ndikukuuzani, Abulahamu asanakhaleko, ine n’kuti ndilipo kale.”+ Akolose 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso, iye ali patsogolo pa zinthu zina zonse,+ ndipo zinthu zina zonse zinakhalapo kudzera mwa iye.+
15 (Yohane anachitira umboni za iye, moti anali kuchita kufuula kuti: “Amene akubwera m’mbuyo mwangamu wandipitirira ine, chifukwa anakhalapo ine ndisanabadwe.”)+
17 Ndiponso, iye ali patsogolo pa zinthu zina zonse,+ ndipo zinthu zina zonse zinakhalapo kudzera mwa iye.+