-
Machitidwe 19:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Koma iwo atazindikira kuti iye ndi Myuda, onse pamodzi anafuula kwa maola pafupifupi awiri kuti: “Wamkulu ndi Atemi mulungu wa Aefeso!”
-