Machitidwe 19:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma iwo atazindikira kuti iye ndi Myuda, onse pamodzi anafuula kwa maola pafupifupi awiri kuti: “Wamkulu+ ndi Atemi mulungu wa Aefeso!”
34 Koma iwo atazindikira kuti iye ndi Myuda, onse pamodzi anafuula kwa maola pafupifupi awiri kuti: “Wamkulu+ ndi Atemi mulungu wa Aefeso!”