-
Machitidwe 19:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Zimene zachitika lerozi nʼzoopsa chifukwa tingathe kuimbidwa nazo mlandu woukira boma. Palibiretu chifukwa chomveka chimene tingapereke pa chipolowe chimene chachitikachi.”
-