-
Machitidwe 19:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Chifukwa kunena zoona, kuopsa kwa zimene zachitika lerozi n’kwakuti angathe kutiimba nazo mlandu woukira boma. Palibiretu chifukwa chomveka chimene tingapereke pa chipolowe chimene chachitikachi.”
-