Machitidwe 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndinkatumikira Ambuye ngati kapolo modzichepetsa kwambiri,+ ndi misozi komanso ndi mayesero amene ndinakumana nawo chifukwa cha ziwembu za Ayuda.
19 Ndinkatumikira Ambuye ngati kapolo modzichepetsa kwambiri,+ ndi misozi komanso ndi mayesero amene ndinakumana nawo chifukwa cha ziwembu za Ayuda.